April 25– May 1
YOBU 33-37
Nyimbo 50 ndi Pemphelo
Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Bwenzi Lenileni Limapeleka Uphungu Wolimbikitsa”: (Mph. 10)
Yobu 33:1-5—Elihu anamulemekeza Yobu (w95-CN 2/15 29 ndime 3-5)
Yobu 33:6, 7—Elihu anali wodzicepetsa ndi wokoma mtima (w95-CN 2/15 29 ndime 3-5)
Yobu 33:24, 25—Elihu analimbikitsa Yobu ngakhale pomupatsa uphungu (w11-CN 4/1 23 ndime 3; w09-CN 4/15 4 ndime 8)
Kufufuza Cuma Cakuuzimu: (Mph. 8)
Yobu 33:24, 25—Kodi “dipo” limene Elihu anachula liyenela kuti linali ciani? (w11-CN 4/1 23 ndime 3-5)
Yobu 34:36—Kodi Yobu anayesedwa mpaka kufika pati? Nanga zimenezi zitiphunzitsa ciani? (w94-CN 11/15 17 ndime 10)
Kodi kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwandiphunzitsa ciani za Yehova?
Ndi mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingagwilitsile nchito mu ulaliki?
Kuŵelenga Baibulo: Yobu 33:1-25 (Mph. 4 kapena zocepelapo)
KUONJEZELA LUSO LANU MU ULALIKI
Ulendo Woyamba: Gaŵilani kapepala koitanila anthu ku msonkhano wacigawo wa 2016, poseŵenzetsa ulaliki wacitsanzo. (Mph. 2 kapena zocepelapo)
Ulendo Wobwelelako: fg phunzilo 12 ndime 4-5. Citani citsanzo ca mmene tingacitile ulendo wobwelelako kwa munthu amene anatenga kapepala ka ciitano ka msonkhano wacigawo. Ndiyeno yalani maziko a ulendo wina wobwelelako. (Mph. 4 kapena zocepelapo)
Phunzilo la Baibulo: jl phunzilo 11. Ndiyeno limbikitsani wophunzila Baibulo kuti akapezeke pa msonkhano wacigawo umene ukubwela. (Mph. 6 kapena zocepelapo)
UMOYO WATHU WACIKRISTU
“Zikumbutso za Msonkhano Wacigawo”: (Mph. 8) Nkhani. Onetsani vidiyo yakuti, Zikumbutso za Msonkhano Wacigawo (Pitani pa tv.pr418.com ndi kuona polemba kuti VIDEO ON DEMAND > OUR ACTIVITIES). Limbikitsani onse kuti akonzekele bwino n’colinga cakuti akapezeke pa msonkhano masiku onse atatu. Kambani makonzedwe amene mpingo wapanga a mmene mudzagaŵilila tumapepala twa ciitano.
Zosoŵa za pampingo: (Mph. 7)
Phunzilo la Baibulo la Mpingo: ia mutu 14 ndime 1-13 (Mph. 30)
Kubweleza Mfundo Zimene Taphunzila ndi Kufotokoza Zimene Tidzaphunzila Mlungu Wotsatila (Mph. 3)
Nyimbo 21 ndi Pemphelo