Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

April 4-10

YOBU 16-20

April 4-10
  • Nyimbo 79 ndi Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Limbikitsani Ena ndi Mau Abwino”: (Mph. 10)

    • Yobu 16:4, 5—Zokamba zathu ziyenela kulimbikitsa ena (w90-CN 3/15 27 ndime 1-2)

    • Yobu 19:2—Mau oipa a Bilidadi anacititsa Yobu kulila mosautsidwa mtima (w06-CN 3/15 15 ndime 6; w94-CN 10/1 32)

    • Yobu 19:25—Ciyembekezo ca kuuka kwa akufa cinalimbikitsa Yobu pamene anakumana ndi mayeselo (w06-CN 3/15 15 ndime 5; it-2 E 735 ndime 2-3)

  • Kufufuza Cuma Cakuuzimu: (Mph. 8)

    • Yobu 19:20—Kodi Yobu anatanthauza ciani ponena kuti “ndapulumuka ndili nazo nkhama za mano anga [khungu la mano anga]”? (w06-CN 3/15 15 ndime 1; it-2 E 977 ndime 1)

    • Yobu 19:26—Kodi Yobu ‘akanaona bwanji Mulungu’ popeza kuti palibe munthu aliyense angaone Yehova? (w94-CN 11/15 19 ndime 17)

    • Kodi kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwandiphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ndi mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingaseŵenzetse mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibulo: Yobu 19:1-23 (Mph. 4 kapena zocepelapo)

KUONJEZELA LUSO LANU MU ULALIKI

  • Konzekelani Maulaliki a Mwezi Uno (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani mavidiyo a maulaliki acitsanzo, ndipo kambilanani mfundo zake. Ngati n’zosatheka kuonelela mavidiyo, ofalitsa aluso acite zitsanzo. Limbikitsani ofalitsa kukonza ulaliki wao.

UMOYO WATHU WACIKRISTU

  • Nyimbo 42

  • Mbali Yatsopano Yoyambitsila Makambilano”: (Mph. 10) Kukambilana. Limbikitsani onse kuseŵenzetsa mbali yakuti “Kodi Baibulo Limakamba Ciani?” poyambitsa makambilano amene angawathandize kuyambitsa phunzilo la Baibulo.

  • Mafunso Ocokela kwa Aŵelengi: (Mph. 5) Nkhani yokambidwa ndi mkulu yocokela mu Nsanja ya Mlonda ya February 15, 2015, tsamba 30, ndime 4-6.

  • Phunzilo la Baibulo la Mpingo: ia mutu 12 ndime 13-25, ndi kubwelelamo pa tsa. 107 (Mph. 30)

  • Kubweleza Mfundo Zimene Taphunzila ndi Kufotokoza Zomwe Tidzaphunzila Mlungu Wotsatila (Mph. 3)

  • Nyimbo 65 ndi Pemphelo