Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

April 10-16

YEREMIYA 22-24

April 10-16
  • Nyimbo 52 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Kodi Muli na ‘Mtima Wodziŵa’ Yehova?”: (10 min.)

    • Yer. 24:1-3—Yehova anayelekezela anthu na nkhuyu (w13 3/15 peji 8 pala. 2)

    • Yer. 24:4-7—Nkhuyu zabwino zinali kuimila anthu a mtima womvela ndi wolabadila (w13 3/15 peji 8 pala. 4)

    • Yer. 24:8-10—Nkhuyu zowola zinaimila anthu a mtima wopanduka ndi wosamvela (w13 3/15 peji 8 pala. 3)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Yer. 22:30—N’cifukwa ciani lamulo limeneli silinaletse Yesu Khristu kutenga mpando wacifumu wa Davide? (w07 3/15 peji 10 pala. 9)

    • Yer. 23:33—Kodi “katundu wolemetsa” wa Yehova n’ciani? (w07 3/15 peji 11 pala. 1)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Yer. 23:25-36

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 mineti kapena kucepelapo)g17.2 nkhani ya pacikuto—Yalani maziko a ulendo wobwelelako.

  • Ulendo Wobwelelako: (4 mineti kapena kucepelapo) g17.2 nkhani ya pacikuto—Yalani maziko a ulendo wobwelelako wotsatila.

  • Phunzilo la Baibo: (6 mineti kapena kucepelapo) lv peji 5 mapala. 1-2—Onetsani mmene mungam’fikile pamtima wophunzila.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU