YEREMIYA 22-24
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU |Kodi Muli na “Mtima Wodziŵa” Yehova?
Yehova anayelekezela anthu na nkhuyu
24:5
-
Ayuda amene anakhalabe okhulupilika mu ukapolo ku Babulo anali monga nkhuyu zabwino
24:8
-
Mfumu yosakhulupilika Zedekiya, ndi ena amene anacita zoipa anali monga nkhuyu zowola
Tingacite ciani kuti tikhale na “mtima wodziŵa” Yehova?
24:7
-
Yehova adzatipatsa ‘mtima womudziŵa’ ngati tiphunzila Mau ake na kuwatsatila
-
Tifunika kusanthula mtima wathu ndi kunyula maganizo na zilako-lako zowononga ubale wathu na Yehova