Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

April 2-8

MATEYU 26

April 2-8
  • Nyimbo 19 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Pasika na Cikumbutso—Kulingana na Kusiyana Kwake”: (10 min.)

    • Mat. 26:17-20—Yesu anadya Pasika yotsiliza na atumwi ake (“Cakudya ca pa Pasikanwtsty zithunzi)

    • Mat. 26:26—Mkate wa pa Cikumbutso umaimila thupi la Yesu (“ukuimilanwtsty mfundo younikila)

    • Mat. 26:27, 28—Vinyo wa pa Cikumbutso umaimila ‘magazi a pangano’ a Yesu (“magazi a panganonwtsty mfundo younikila)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Mat. 26:17—N’cifukwa ciani tingakambe kuti Nisani 13 ni “tsiku loyamba la cikondwelelo ca mikate yopanda cofufumitsa”? (“Pa tsiku loyamba la cikondwelelo ca mikate yopanda cofufumitsanwtsty mfundo younikila)

    • Mat. 26:39—N’ciani ciyenela kuti cinasonkhezela Yesu kupemphela kuti: “kapu iyi indipitilile”? (“kapu iyi indipitilile” nwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mat. 26:1-19

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 20

  • Zofunikila za Mpingo: (8 min.)

  • Khala Bwenzi la Yehova—Dipo: (7 min.) Tambitsani vidiyo imeneyi. Pambuyo pake, itanani ana amene munasankha kuti abwele ku pulatifomu, na kuwafunsa mafunso aya: N’cifukwa ciani anthu amadwala, kukalamba, na kufa? Kodi Yehova watipatsa ciyembekezo canji? Kodi iwe ufuna ukaonane na ndani m’paradaiso?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 15

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 74 na Pemphelo