April 9-15
MATEYU 27-28
Nyimbo 69 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Pitani Mukapange Ophunzila—Cifukwa ciani, Kuti, ndipo Motani?”: (10 min.)
Mat. 28:18—Yesu ali na ulamulilo waukulu (w04 7/1 peji 8 pala. 4)
Mat. 28:19—Yesu analamula kuti tilalikile na kuphunzitsa anthu pa dziko lonse (“mukaphunzitse anthu” “anthu a mitundu yonse” nwtsty mfundo zounikila)
Mat. 28:20—Tifunika kuthandiza anthu kudziŵa na kuseŵenzetsa zonse zimene Yesu anatiphunzitsa (“kuwaphunzitsa” nwtsty mfundo younikila)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Mat. 27:51—Kodi kung’ambika pakati kwa nsalu yochinga kunatanthauza ciani? (“nsalu yochinga,” “nyumba yopatulika” nwtsty mfundo zounikila)
Mat. 28:7—Kodi mngelo wa Yehova anawalemekeza bwanji azimayi amene anapita ku manda a Yesu? (“mukauze ophunzila ake kuti wauka kwa akufa” nwtsty mfundo younikila)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mat. 27:38-54
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.
Vidiyo ya Kubwelelako Koyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Nkhani: (6 min. olo kucepelapo) g17.2 peji 14—Mutu: Kodi Yesu anafera pamtanda?
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Kulalikila na Kuphunzitsa—N’kofunika pa Nchito Yopanga Ophunzila”: (15 min.) Kukambilana. Pokambilana nkhaniyi, tambitsani vidiyo yakuti Pitilizani Kulalikila “Mwakhama”—Ulaliki Wamwayi, Kunyumba ndi Nyumba, ndi yakuti Pitilizani Kulalikila “Mwakhama”—Ulaliki Wapoyela, Kupanga Ophunzila.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 16
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 73 na Pemphelo