April 29–May 5
2 AKORINTO 1-3
Nyimbo 44 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova ni ‘Mulungu Amene Amatitonthoza M’njila Iliyonse’”: (10 min.)
[Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Akorinto Waciŵili.]
2 Akor. 1:3—Yehova ni “Tate wacifundo cacikulu” (w17.07 13 ¶4)
2 Akor. 1:4—Timatonthoza ena cifukwa nafenso Yehova amatitonthoza (w17.07 15 ¶14)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
2 Akor. 1:22—Kodi “cikole” komanso “cidindo” cimene Mkhristu aliyense wodzozedwa amalandila kucokela kwa Mulungu ciani? (w16.04 32)
2 Akor. 2:14-16—Kodi mtumwi Paulo ayenela kuti anatanthauza ciani pamene anakamba za ‘kuguba pa cionetselo conyadilila kupambana’? (w10 8/1 23)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) 2 Akor. 3:1-18 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 6)
Phunzilo la Baibo: (5 min. olo kucepelapo) bhs 52-53 ¶3-4 (th phunzilo 8)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Pitilizani Kulandila Maphunzilo Aumulungu”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Olemela Mwauzimu Cifukwa Cophunzitsidwa na Yehova.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 64
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 130 na Pemphelo