Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

April 8-14

1 AKORINTO 10-13

April 8-14
  • Nyimbo 30 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Yehova ni Wokhulupilika”: (10 min.)

    • 1 Akor. 10:13—Yehova sacita kutisankhila mayeselo amene timakumana nawo (w17.02 29-30)

    • 1 Akor. 10:13—Mayeselo amene timakumana nawo ‘amagwelanso anthu ena’

    • 1 Akor. 10:13—Yehova adzatithandiza kupilila mayeselo alionse amene tingakumane nawo, malinga ngati timudalila

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • 1 Akor. 10:8—N’cifukwa ciani vesiyi imakamba kuti Aisraeli amene anaphedwa tsiku limodzi cifukwa cocita dama anali 23,000, pamene pa Numeri 25:9 pamati anali 24,000? (w04 4/1 29)

    • 1 Akor. 11:5, 6, 10—Kodi mlongo afunika kuvala cakumutu pamene akucititsa phunzilo la Baibo ali pamodzi na wofalitsa wammuna? (w15 2/15 30)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) 1 Akor. 10:1-17 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 25

  • ‘Ziwalo za Thupi . . .  N’zofunika.’ (1 Akor. 12:22): (10 min.) Tambitsani vidiyoyi..

  • Kodi Mudzakonzekela Bwanji Cikumbutso?”: (5 min.) Nkhani. Limbikitsani onse kuti pa nyengo ya Cikumbutso, azisinkha-sinkha na kukulitsa ciyamikilo cawo pa cikondi cimene Yehova na Yesu anationetsa.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 62

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 31 na Pemphelo