UMOYO NA UTUMIKI WATHU–KABUKU KA MISONKHANO April 2020

Makambilano Acitsanzo

Mpambo wa makambilano onena za colinga ca Mulungu kwa anthu, ndiponso mmene cidzakwanilitsidwila.

April 6-12

Kodi mudzakonzekeletsa bwanji mtima wanu kaamba ka Cikumbutso ca imfa ya Khristu?

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yakobo na Labani Acita Pangano la Mtendele

Kodi mungacite ciani kuti mukhalebe kapena kubwezeletsa mtendele na ena?

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Mukulimbikila kuti Mupeze Madalitso?

Kodi ndimwe ofunitsitsa kucita ciani kuti mulandile madalitso a Mulungu?

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Kodi Cofunika Koposa kwa Ine N’ciani?

Kodi nchito imene mumagwila ionetsa kuti mumaika zinthu zotani patsogolo?

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Zotulukapo Zoopsa za Mayanjano Oipa

Kodi tingadziŵe bwanji ngati munthu wina ni bwenzi labwino kapena ayi?

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

“Cotsani Milungu Yacilendo”

Kodi tingacite ciani kuti tikondweletse Yehova kuti tipewe kuvutitsidwa na ziŵanda?