Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 31

Yakobo na Labani Acita Pangano la Mtendele

Yakobo na Labani Acita Pangano la Mtendele

31:44-53

N’cifukwa ciani Yakobo na Labani anaunjika mulu wa miyala?

  • Mulu wa miyalawo unali umboni kwa odutsa wakuti iwo anacita pangano la mtendele

  • Unali kuwakumbutsa kuti Yehova anali kuyang’ana kuti aone ngati iwo akusunga pangano lawo la mtendele

Masiku ano, Yehova amafuna kuti tizikhala mwamtendele ndi abale na alongo athu. Kodi kucita zinthu zitatu zotsatilazi kungatithandize bwanji kukhazikitsa mtendele kapena kuubwezeletsa?

  • Kukambilana.Mat. 5:23, 24

  • Kukhululukilana na mtima wonse.Akol. 3:13

  • Kukhala woleza mtima.Aroma 12:21