Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

April 20-26

GENESIS 32-33

April 20-26
  •  Nyimbo 21 na Pemphelo

  •  Mawu Oyamba (1 min.)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Kodi Mukulimbikila kuti Mupeze Madalitso?”: (10 min.)

    • Gen. 32:24—Yakobo anagwebana na mngelo (w03 8/15 25 ¶3)

    • Gen. 32:25, 26—Yakobo sanaleke kugwebana na mngeloyo kufikila atadalitsidwa (it-2 190)

    • Gen. 32:27, 28—Yakobo anadalitsidwa cifukwa ca kulimbikila kwake (it-1 1228)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)

    • Gen. 32:11, 13-15—Tingatengele bwanji khama la Yakobo pa nkhani yokhazikitsa mtendele? (w10 6/15 22 ¶10-11)

    • Gen. 33:20—N’cifukwa ciani Yakobo anacha guwa lansembe “Mulungu, Mulungu wa Isiraeli”? (it-1 980)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova Mulungu, ulaliki, kapena mbali ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Gen. 32:1-21 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU