Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

April 27–May 3

GENESIS 34-35

April 27–May 3
  •  Nyimbo 28 na Pemphelo

  •  Mawu Oyamba (1 min.)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Zotulukapo Zoopsa za Mayanjano Oipa”: (10 min.)

    • Gen. 34:1—Mobweleza-bweleza Dina anali kupita kukaceza na ana aakazi acikanani (w97 2/1 30 ¶4)

    • Gen. 34:2—Sekemu anagwilila Dina (lvs 124 ¶14)

    • Gen. 34:7, 25—Simiyoni na Levi anapha Sekemu pamodzi na mwamuna aliyense wa mumzindawo (w09 9/1 21 ¶1-2)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)

    • Gen. 35:8—Kodi Debora anali ndani? Nanga tingaphunzile ciani kwa iye? (it-1 600 ¶4)

    • Gen. 35:22-26—Tidziŵa bwanji kuti kukhala pa mzele wa makolo a Mesiya sikunadalile kukhala woyamba kubadwa? (w17.12 14)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova Mulungu, ulaliki, kapena mbali ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Gen. 34:1-19 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU