UMOYO NA UTUMIKI WATHU–KABUKU KA MISONKHANO August 2016
Maulaliki a Citsanzo
Maulaliki a citsanzo ogaŵila Galamukani! ndi Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya. Seŵenzetsani maulaliki a citsanzo pokonza ulaliki wanu.
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Khalanibe m’Malo Otetezeka a Wam’mwambamwamba
Kodi “malo otetezeka” a wam’mwambamwamba n’ciani? Nanga amatithandiza bwanji kukhala otetezeka? (Salimo 91)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Kunola Luso Lathu mu Ulaliki —Kuthandiza Ophunzila Baibulo Kuti Adzipeleke ndi Kubatizika
N’cifukwa ciani kudzipeleka ndi kubatizidwa n’kofunika kwambili? Nanga mungathandize bwanji ophunzila Baibulo anu kukwanilitsa zolinga zimenezi?
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Amabala Zipatso Ngakhale ni Okalamba
Mavesi a Salimo 92 agogomeza mfundo yakuti acikulile angathe kubalabe zipatso zauzimu.
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Yehova Amadziŵa Kuti Ndife Fumbi
Mu Salimo 103, Davide anaseŵenzetsa mafanizo pofotokoza kukula kwa cifundo ca Yehova.
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Yamikani Yehova”
Mavesi a mu Salimo 106 angakuthandizeni kukhala na mtima wokonda kuyamikila Yehova nthawi zonse.
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Yehova Ndidzamubwezela Ciani?”
Kodi wamasalimo anaonetsa bwanji kuti anali kufuna kuyamikila Yehova? (Salimo 116)
UMOYO WATHU WACIKHIRISTU
Phunzitsani Coonadi
Phunzitsani anthu mfundo yomveka bwino ya coonadi ca m’Baibulo pogwilitsila nchito ulaliki wa citsanzo watsopano umenewu.
UMOYO WATHU WACIKHIRISTU
Kampeni Yapadela Yogaŵila Nsanja ya Mlonda mu September
Nsanja ya Mlonda imeneyi idzakamba za citonthozo ndi mmene Mulungu amatitonthozela.