Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

August 22-28

MASALIMO 106–109

August 22-28
  • Nyimbo 2 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Yamikani Yehova”: (Mph. 10)

    • Sal. 106:1-3—Yehova ni woyenela kumuyamikila (w15 1/15 tsa. 8 ndime 1; w02 6/1-CN, tsa. 18 ndime 19)

    • Sal. 106:7-14, 19-25, 35-39—Aisiraeli analeka kuyamikila Yehova ndipo anakhala osakhulupilika (w15 1/15 8-9 ndime 2-3; w01 6/15-CN, tsa. 13 ndime 1-3)

    • Sal. 106:4, 5, 48—Tili na zifukwa zambili zoyamikila Yehova (w11 10/15-CN, tsa. 5 ndime 7; w03 12/1-CN tsa. 15-16 ndime 3-6)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu (Mph. 8)

    • Sal. 109:8—Kodi Mulungu anakonzelatu zakuti Yudasi adzapeleke Yesu n’colinga cakuti akwanilitse ulosi? (w00 12/15-CN, tsa. 24 ndime 20; it-1 857-858)

    • Sal. 109:31—Kodi Yehova amaima bwanji “kudzanja lamanja la munthu wosauka”? (w06 9/1-CN, tsa. 14 ndime 8)

    • Kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ningaseŵenzetse mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibulo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Sal. 106: 1-22

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHIRISTU

  • Nyimbo 94

  • Yehova Adzatisamalila (Sal. 107:9): (Mph. 15) Kukambilana. Coyamba tambitsani vidiyo yakuti Yehova Adzatisamalila. (Pitani pa jw.org, ndi kuona pa MABUKU > MAVIDIYO.) Pemphani omvela kuti akambe zimene aphunzilapo. Ngati n’zosatheka kuonelela vidiyo, kambilanani mfundo za m’magazini iyi: w05 10/15-CN, masa. 8-9, nkhani yakuti: “Yehova Sadzakusiyani Konse.”

  • Phunzilo la Baibulo la Mpingo: (Mph. 30) ia mutu 22 ndime 14-24, ndi kubwelelamo pa tsa. 194

  • Kubwelelamo ndi Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3)

  • Nyimbo 149 na Pemphelo