August 29– September 4
MASALIMO 110–118
Nyimbo 61 na Pemphelo
Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Yehova Ndidzamubwezela Ciani?”: (Mph. 10)
Sal. 116:3, 4, 8—Yehova anapulumutsa wamasalimo ku imfa (w87 3/15-E, tsa. 24 ndime 5)
Sal. 116:12—Wamasalimo anafuna kuonetsa kuti amayamikila Yehova (w09 7/15-CN, tsa. 29 ndime 4-5; w98 12/1-CN, tsa. 24 ndime 3)
Sal. 116:13, 14, 17, 18—Wamasalimo anali wofunitsitsa kukwanilitsa udindo wake kwa Yehova (w10 4/15-CN, tsa. 27, bokosi)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 8)
Sal. 110:4—Kodi vesi imeneyi ikamba za lumbilo liti? (w14 10/15 tsa. 11 ndime 15-17; w06 9/1-CN, tsa. 14 ndime 1)
Sal. 116:15—Pokamba nkhani ya malilo, n’cifukwa ciani si bwino kugwilitsila nchito lemba la Salimo 116:15 pofotokoza za munthu womwalilayo? (w12 5/15-CN, tsa. 22 ndime 2)
Kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?
Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ningaseŵenzetse mu ulaliki?
Kuŵelenga Baibulo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Sal. 110:1–111:10
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya tsa. 16—Yalani maziko a ulendo wobwelelako.
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya tsa. 17—Yalani maziko a ulendo wina wobwelelako.
Phunzilo la Baibulo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) bh masa. 179-181 ndime 17-19—Thandizani wophunzila kuona mmene angaseŵenzetsele mfundo za m’nkhani imeneyo.
UMOYO WATHU WACIKHIRISTU
Nyimbo 82
“Phunzitsani Coonadi”: (Mph. 7) Kukambilana.
“Kampeni Yapadela Yogaŵila Nsanja ya Mlonda mu September”: (Mph. 8) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yoyamba ya citsanzo ca ulaliki mu September. Ndiyeno kambilanani zimene mwaphunzilapo. Limbikitsani ofalitsa kuti adzagwileko nchito yapadela imeneyi ndi kutengako upainiya wothandiza.
Phunzilo la Baibulo la Mpingo: (Mph. 30) ia mutu 23 ndime 1-14
Kubwelelamo ndi Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3)
Nyimbo 144 na Pemphelo
Cikumbutso: Lizani nyimbo yonse kamodzi, ndiyeno mpingo uyimbile pamodzi nyimboyo.