Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MASALIMO 92-101

Amabala Zipatso Ngakhale ni Okalamba

Amabala Zipatso Ngakhale ni Okalamba

92:12

Mitengo ina ya kanjedza imakhala zaka zoposa 100, ndipo imabalabe zipatso

Acikulile amabala zipatso zauzimu mwa . . .

92:13-15

  • kupemphelela ena

  • kuphunzila Baibulo

  • kupezeka pamisonkhano na kuyankhapo

  • kuuzako ena zinthu zimene adziŵa

  • kulalikila modzipeleka