August 20-26
LUKA 21-22
Nyimbo 27 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Cipulumutso Canu Cikuyandikila”: (10 min.)
Luka 21:25—Pa cisautso cacikulu padzacitika zinthu zocititsa mantha (kr peji 226 pala. 9)
Luka 21:26—Adani a Yehova adzacita mantha
Luka 21:27, 28—Kubwela kwa Yesu kudzatanthauza cipulumutso kwa anthu okhulupilika (w16.01 mape 10-11 pala. 17; w15 7/15 mape 17-18 pala. 13)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Luka 21:33—Kodi zimene Yesu anakamba pa vesiyi zitanthauza ciani? (“Kumwamba ndi dziko lapansi zidzacoka,” “mau anga sadzacoka ayi” nwtsty mfundo zounikila)
Luka 22:28-30—Kodi Yesu anacita pangano lanji, nanga anacita na ndani? Kodi panganolo lidzatheketsa ciani? (w14 10/15 mape 16-17 mapa. 15-16)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Luka 22:35-53
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Onetsani mmene mungayankhile pa zimene anthu a m’gawo lanu amakamba posafuna kulalikidwa.
Kubwelelako Koyamba: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na akambilano acitsanzo. Onetsani mmene mungacitile ngati mwininyumba ni wotangwanika.
Vidiyo ya Kubwelelako Kaciŵili: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (15 min.)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 34
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 41 na Pemphelo