Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

August 27–September 2

LUKA 23-24

August 27–September 2
  • Nyimbo 130 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Muzikhala Okonzeka Kukhululukila Ena”: (10 min.)

    • Luka 23:34—Yesu anakhululukila asilikali aciroma amene anamukhomelela pa mtengo (cl peji 297 pala. 16)

    • Luka 23:43—Yesu anakhululukila munthu wocita zoipa (g 2/08 peji 11 mapa. 5-6)

    • Luka 24:34—Yesu anakhululukila Petulo (cl mape. 297-298 mapa. 17-18)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Luka 23:31—Kodi Yesu ayenela kuti anali kukamba za ndani pa vesiyi? (“pamene mtengo uli wauŵisi, . . . mtengowo ukadzaumanwtsty mfundo younikila)

    • Luka 23:33—Kodi zinthu zakale zofukulidwa zionetsa bwanji kuti misomali anali kuiseŵenzetsa popha munthu mwa kum’khomelela pamtengo? (“Msomali mu fupa la kadendenenwtsty zithunzi)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Luka 23:1-16

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Kubwelelako Kaciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani cofalitsa cophunzitsila Baibo ca mu Thuboksi yathu, mogwilizana na zosoŵa za mwininyumba.

  • Kubwelelako Kacitatu: (3 min. olo kucepelapo) Sankhani mwekha lemba, ndipo gaŵilani cofalitsa cophunzitsila Baibo.

  • Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) fg phunzilo 4 mapa. 3-4

UMOYO WATHU WACIKHRISTU