August 6-12
LUKA 17-18
Nyimbo 18 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Muzionetsa Kuyamikila”: (10 min.)
Luka 17:11-14—Yesu anacilitsa anthu 10 akhate (“amuna 10 akhate” nwtsty mfundo zounikila pa Luka 17:12, 14 “mukadzionetse kwa ansembe”)
Luka 17:15, 16—Wakhate mmodzi cabe ndiye anabwelela kukayamikila Yesu
Luka 17:17, 18—Nkhani imeneyi itiunikila kufunika koonetsa kuyamikila (w08 8/1 mape. 14-15 mapa. 8-9)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Luka 17:7-10—Kodi mfundo ya Yesu m’fanizo ili ni yotani? (“opanda pake” nwtsty mfundo younikila pa Luka 17:10)
Luka 18:8—Ni cikhulupililo cotani cimene Yesu anali kutanthauza pa vesiyi? (“cikhulupililo” nwtsty mfundo younikila)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Luka 18:24-43
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Kubwelelako Koyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.
Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) fg phunzilo 4 mapa. 1-2
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Kumbukilani Mkazi wa Loti”: (15 min.) Kukambilana.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 32
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 117 na Pemphelo