UMOYO NA UTUMIKI WATHU–KABUKU KA MISONKHANO August 2019
Makambilano Acitsanzo
Makambilano a citsanzo otsatizana-tsatizana pa malonjezo a Mulungu odalilika.
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mulungu Sanatipatse Mzimu Wamantha”
Tingakhale olimba mtima pokumana na mayeselo ngati tidalila mphamvu za Mulungu.
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Muziyanjana na Anthu Okonda Yehova
Anthu amene timayanjana nawo angatilimbikitse kucita zinthu zabwino kapena zoipa.
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kuika Akulu”
Amene amatsogolela mu mpingo wacikhristu amaikidwa mogwilizana na mfundo za m’Baibo.
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Acinyamata—Khalani “Odzipeleka pa Nchito Zabwino”
Kodi acinyamata angacite ciani kuti akwanilitse colinga cawo cocita upainiya wothandiza kapena wanthawi zonse?
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Kondani Cilungamo, Danani Nako Kusamvela Malamulo
Tingaonetse bwanji kuti timakonda cilungamo na kudana na kusamvela malamulo?
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Limbikilani Kuti Mukaloŵe mu Mpumulo wa Mulungu
Kodi tingaloŵe bwanji mu mpumulo wa Mulungu? Nanga tingacite ciani kuti tikhalebe mmenemo?
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Nchito Zabwino Zimene Sizidzaiŵalidwa
Kodi mungacite ciani kuti muyenelele kukatumikila Yehova pa Beteli?