August 26–September 1
AHEBERI 4-6
Nyimbo 5 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Limbikilani Kuti Mukaloŵe mu Mpumulo wa Mulungu”: (10 min.)
Aheb. 4:1, 4—Lidziŵeni tsiku la mpumulo wa Mulungu (w11 7/15 24-25 ¶3-5)
Aheb. 4:6—Muzimvela Yehova (w11 7/15 25 ¶6)
Aheb. 4:9-11—Pewani kukhala na mzimu wodzidalila (w11 7/15 28 ¶16-17)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Aheb. 4:12—Kodi “mawu a Mulungu” ochulidwa pa lembali n’ciani? (w16.09 13)
Aheb. 6:17, 18—Kodi “zinthu ziŵili zosasinthika” zochulidwa m’mavesiwa n’ciani? (it-1 1139 ¶2)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Aheb. 5:1-14 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 6)
Phunzilo la Baibo: (5 min. olo kucepelapo) lvs 228-229 ¶7-8 (th phunzilo 12)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Nchito Zabwino Zimene Sizidzaiŵalidwa”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Dzipelekeni Kukacita Utumiki wa pa Beteli.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 81
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 12 na Pemphelo