AHEBERI 4-6
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU |Limbikilani Kuti Mukaloŵe mu Mpumulo wa Mulungu
4:11
Tingaloŵe mu mpumulo wa Yehova mwa kugwila nchito mogwilizana na cifunilo cake cimene cikuvumbulidwa kupitila m’gulu lake. Tifunika kudzifunsa kuti: ‘Kodi nimatani nikalandila uphungu? Kodi nimamvela bwanji ngati kamvedwe ka Malemba kasinthidwa?’
Ni zinthu ziti mu umoyo zimene zimayesa kumvela kwanga?