December 12-18
YESAYA 6-10
Nyimbo 116 na Pemphelo
Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Ulosi wa Mesiya Umene Unakwanilitsika”: (Mph. 10)
Yes. 9:1, 2—Ulaliki wake wapoyela ku Galileya unanenedwelatu (w11 8/15 tsa. 10 ndime 13; ip-1 tsa. 124-126 ndime 13-17)
Yes. 9:6—Adzakhala na maudindo ambili osiyana-siyana (w14 2/15 tsa. 12 ndime 18; w07 5/15 tsa. 6)
Yes. 9:7—Ulamulilo wake udzabweletsa mtendele wa zoona na cilungamo (ip-1 tsa. 132 ndime 28-29)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 8)
Yes. 7:3, 4—N’cifukwa ciani Yehova anapulumutsa Mfumu yoipa Ahazi? (w06 12/1 tsa. 9 ndime 4)
Yes. 8:1-4—Ulosi umenewu unakwanilitsika bwanji? (it-1 1219; ip-1 tsa. 111-112 ndime 23-24)
Kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani ine za Yehova?
Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno zimene ine ningaseŵenzetse mu ulaliki?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Yes. 7:1-17
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) g16.6 nkhani ya pacikuto
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) g16.6 nkhani ya pacikuto
Phunzilo la Baibo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) lv 34 tsa. 18—Onetsani mmene tingam’fikile pamtima wophunzila.
UMOYO WATHU WACIKHIRISTU
“Ine Ndilipo! Nditumizeni.” (Yes. 6:8) (Mph. 15) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Kukatumikila ku Malo Osoŵa. (Yendani ku mavidiyo pa MISONKHANO NA UTUMIKI WATHU).
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30.) kr nkhani. 5 ndime 10-17, na bokosi pa tsamba 53”
Kubwelelamo na Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3)
Nyimbo 150 na Pemphelo
Cikumbutso: Lizani nyimbo yonse kamodzi, ndiyeno mpingo uyimbile pamodzi nyimboyo.