December 19-25
YESAYA 11-16
Nyimbo 143 na Pemphelo
Omau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Dziko Lapansi Lidzadzala na Ŵanthu Odziwa Yehova”: (Mph. 10)
Yes. 11:3-5—Kudzakhala cilungamo mpaka muyaya (ip-1 160-161 ndime 9-11)
Yes. 11:6-8—Anthu na vinyama adzakhala pamtendele (w12 9/15 9-10 ndime 8-9)
Yes. 11:9—Mitundu yonse ya anthu idzaphunzila njila za Yehova (w16.06 tsa. 8 ndime 9; w13 6/1 7)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 8)
Yes. 11:1, 10—Kodi Yesu Khiristu angakhale bwanji “muzu wa Jese” na nthambi imene inamphuka “pacitsa ca Jese”? (w06 12/1 tsa. 9 ndime 6)
Yes. 13:17—Kodi Amedi anasuliza bwanji siliva ndipo sanakondwele na golide m’njila yanji? (w06 12/1 tsa.10 ndime 10)
Kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani ine za Yehova?
Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno zimene ine ningaseŵenzetse mu ulaliki?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Yes. 13:17–14:8
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) Yobu 34:10—Phunzitsani Coonadi.
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Mlal. 8:9; 1 Yoh. 5:19—Phunzitsani Coonadi.
Phunzilo la Baibo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) lv tsa. 54 ndime 9—Onetsani mmene tingam’fikile pamtima wophunzila.
UMOYO WATHU WACIKHIRISTU
“Maphunzilo Aumulungu Amagonjetsa Tsankho”: (Mph. 15) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Johny na Gideon: Anali Adani, Tsopano ni Abale (Yendani ku mavidiyo pa KUFUNSA MAFUNSO NA ZOCITIKA)..
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30.) kr nkhani 5 ndime 18-25, bokosi pa tsa. 57
Kubwelelamo na Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3)
Nyimbo 151 na Pemphelo
Cikumbutso: Lizani nyimbo yonse kamodzi, ndiyeno mpingo uyimbile pamodzi.