December 26–January 1
YESAYA 17-23
Nyimbo 123 na Pemphelo
Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Kuseŵenzetsa Mphamvu Mwadyela Kumatayitsa Udindo”: (Mph. 10)
Yes. 22:15, 16—Sebina anaseŵenzetsa udindo wake mwadyela (ip-1 238 ndime 16-17)
Yes. 22:17-22—Yehova anaika Eliyakimu pa udindo wa Sebina (ip-1 238-239 ndime 17-18)
Yes. 22:23-25—Cocitika ca Sebina citiphunzitsa mfundo zofunika (w07 1/15 8 ndime 6; ip-1 240-241 ndime 19-20)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 8)
Yes. 21:1—Ni dela iti imene inachedwa “cipululu ca nyanja?” Nanga n’cifukwa ciani? (w06 12/1 11 ndime 2)
Yes. 23:17, 18—Kodi cuma ca mzinda wa Tulo cinakhala bwanji ‘copatulika kwa Yehova’? (ip-1 253-254 ndime 22-24)
Kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani ine za Yehova?
Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno zimene ine ningaseŵenzetse mu ulaliki?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Yes. 17: 1-14
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) bh—Chulani za kavidiyo kakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? pogaŵila bukuli. (Musacite kutambitsa kavidiyoka.)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) bh—Kuyambitsa phunzilo la Baibo la coimilila pakhomo, na kuyala maziko a ulendo wotsatila.
Phunzilo la Baibo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) lv 150-151 ndime 10-11—Onetsani mmene mungam’fikile pamtima wophunzila.
UMOYO WATHU WACIKHIRISTU
Kodi ‘Mudzakhalabe Maso’?: (Mph. 8) Nkhani yokambiwa na Mkulu yozikidwa mu Nsanja ya Mlonda ya March 15, 2015, masamba 12-16. Limbikitsani aliyense kukhalabe maso monga mlonda amene Yesaya anaona m’masomphenya, na anamwali 5 a m’fanizo la Yesu.—Yes. 21:8; Mat. 25:1-13.
Zimene Gulu Likukwanilitsa: (Mph. 7) Tambitsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Likukwanilitsa ya December.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) kr nkhani 6 ndime 1-7, masa. 58-59”
Kubwelelamo na Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3)
Nyimbo 141 na Pemphelo