YESAYA 17-23
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU |Kuseŵenzetsa Mphamvu Mwadyela Kumatayitsa Udindo
Sebina anali kapitawo “woyang’anila nyumba” ya mfumu, mwacionekele mfumu Hezekiya. Anali waciŵili kwa mfumu, ndipo anali na udindo waukulu.
22:15, 16
-
Sebina anayenela kusamalila zosoŵa za anthu a Yehova
-
Koma iye anacita zinthu mwadyela pofuna ulemelelo
22:20-22
-
Yehova anaika Eliyakimu pa udindo wa Sebina
-
Eliyakimu anapatsiwa “makiyi a nyumba ya Davide” amene anaimila mphamvu na ulamulilo
Ganizilani: Kodi Sebina anafunikila kuseŵenzetsa bwanji udindo wake kuti athandize anthu?