December 5- 11
YESAYA 1-5
Nyimbo 107 na Pemphelo
Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Tiyeni Tipite Kukakwela Phili la Yehova”: (Mph. 10)
[Tambitsani vidiyo ya Mfundo Zokhudza Buku la Yesaya..]
Yes. 2:2, 3—“Phili la nyumba ya Yehova” liimila kulambila koyela (ip-1 tsa. 38-41 ndime 6-11; tsa. 44-45 ndime 20-21)
Yes. 2:4—Olambila Yehova saphunzilanso nkhondo (ip-1 tsa. 46-47 ndime 24-25)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 8)
Yes. 1:8, 9—Kodi mwana mkazi wa ziyoni anasiyidwa bwanji “ngati msasa m’munda wa mpesa”? (w06 12/1 tsa. 8 ndime 5)
Yes. 1:18—Kodi Yehova anatanthauza ciani pamene anati: “Tiyeni tikambilane”? (w06 12/1 tsa. 9 ndime 1; it-2 tsa. 761 ndime 3)
Kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani ine za Yehova?
Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno zimene ine ningaseŵenzetse mu ulaliki?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Yes. 5:1- 13
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Konzekelani Maulaliki a Mwezi Uno: (Mph. 15) Kukambilana kozikidwa pa “Maulaliki a Citsanzo.” Tambitsani vidiyo ya citsanzo iliyonse na kukambilana zimene mwaphunzilapo. Limbikitsani ofalitsa kukonza ulaliki wawo.
UMOYO WATHU WACIKHIRISTU
Zosoŵa za Pampingo: (Mph. 7) Apo ayi, kambilanani mfundo zimene mwaphunzila mu Buku Lapacaka (yb16 tsa. 32 ndime 3 mpaka tsa. 34 ndime 1)
“Kunola Luso Lathu mu Ulaliki— Afikeni Pamtima na Buku Yakuti, ‘Khalanibe m’Cikondi ca Mulungu’”: (Mph. 8) Kukambilana. Limbikitsani amene anapatsidwa nkhani ya mwana wa sukulu ya kucititsa Phunzilo la Baibo mwezi uno kuti akatsatile mfundo zili pa masamba 261-262 m’buku la Sukulu ya Utumiki.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) kr nkhani 5 ndime 1-9
Kubwelelamo na Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3)
Nyimbo 154 na Pemphelo
Cikumbutso: Lizani nyimboyi kamodzi, ndiyeno mpingo uyimbile pamodzi.