Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

December 10-16

MACHITIDWE 12-14

December 10-16
  • Nyimbo 60 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Paulo na Baranaba Apanga Ophunzila Kumadela Akutali”: (10 min.)

    • Mac. 13:2, 3—Yehova anasankha Saulo na Baranaba kuti acite nchito yapadela (bt peji 86 pala. 4)

    • Mac. 13:12, 48; 14:1—Kugwila kwawo nchito mwakhama, kunakhala na zotulukapo zabwino (bt peji 95 pala. 5)

    • Mac. 14:21, 22—Paulo na Baranaba analimbikitsa ophunzila atsopano (w14 9/15 peji 13 mapa. 4-5)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Mac. 12:21-23—Tiphunzilapo ciani pa zimene zinacitikila Herode? (w08 5/15 peji 32 pala. 7)

    • Mac. 13:9—N’cifukwa ciani Saulo anali ‘kuchedwanso Paulo’? (“Saulo, wochedwanso Paulo”, “Paulonwtsty mfundo zounikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mac. 12:1-17

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.

  • Vidiyo ya Kubwelelako Koyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Nkhani: (6 min. olo kucepelapo) bt mape. 78-79 mapa. 8-9—Mutu: Tizipemphelela Okhulupilila Anzathu.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU