Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

December 17-23

MACHITIDWE 15-16

December 17-23
  • Nyimbo 96 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Cigamulo Cozikidwa pa Mawu a Mulungu”: (10 min.)

    • Mac. 15:1, 2—Nkhani ya mdulidwe inakula moti ikanagaŵanitsa mpingo woyambilila wacikhristu (bt mapeji 102-103 pala. 8)

    • Mac. 15:13-20—Cigamulo ca bungwe lolamulila cinali cozikidwa pa Malemba (w12 1/15 peji 5 mapa. 6-7)

    • Mac. 15:28, 29; 16:4, 5—Cigamulo ca bungwe lolamulila cinalimbitsa mipingo (bt peji 123 pala. 18)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Mac. 16:6-9—Kodi nkhaniyi itiphunzitsa ciani za kuwonjezela utumiki wathu? (w12 1/15 peji 10 pala. 8)

    • Mac. 16:37—Kodi mtumwi Paulo anaseŵenzetsa bwanji unzika wake waciroma kuti akwanilitse nchito yolalikila uthenga wabwino? (““ndife Aromanwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mac. 16:25-40

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU