Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

December 24-30

MACHITIDWE 17-18

December 24-30
  • Nyimbo 78 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Tengelani Citsanzo ca Mtumwi Paulo Polalikila na Kuphunzitsa”: (10 min.)

    • Mac. 17:2, 3—Pophunzitsa, Paulo anali kukambilana na anthu mfundo za M’malemba na kuwaonetsa umboni wolembedwa (“anakambilana”, “kusonyeza umboni wolembedwanwtsty mfundo zounikila)

    • Mac. 17:17—Paulo anali kulalikila kulikonse kumene wapeza anthu (“pamsikanwtsty mfundo younikila)

    • Mac. 17:22, 23—Paulo anali kukhala chelu kuti ayale maziko abwino oyambilapo ulaliki (“Kwa Mulungu Wosadziŵikanwtsty mfundo younikila)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Mac. 18:18—Kodi tingati ciani pa lumbilo limene Paulo anapanga? (w08 5/15 peji 32 pala. 5)

    • Mac. 18:21—Tingatengele bwanji citsanzo ca Paulo pamene tiyesa kukwanilitsa zolinga zathu zauzimu? (“Yehova akalolanwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mac. 17:1-15

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 70

  • Lalikilani na Kuphunzitsa Uthenga Wabwino Mokwanila: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Kulambila kwa Pabanja: Paulo—Analalikila Uthenga Wabwino Mokwanila. Pambuyo pake, funsani mafunso aya: Kodi banja limene taona mu vidiyo linazindikila bwanji kuti linafunika kuwonjezela luso mu ulaliki? Kodi iwo anatengela mbali ziti za utumiki kwa mtumwi Paulo? Nanga pothela pake anapeza madalitso anji? Ni mfundo ziti zokhudza kulambila kwa pabanja zimene imwe mungaziseŵenzetse?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 47

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 151 na Pemphelo