December 16-22
CHIVUMBULUTSO 13-16
Nyimbo 55 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Musamaope Zilombo Zoopsa”: (10 min.)
Chiv. 13:1, 2—Cinjoka cinapeleka ulamulilo kwa cilombo ca nyanga 10 na mitu 7 (w12 6/15 8 ¶6)
Chiv. 13:11, 15—Cilombo ca nyanga ziŵili cinapeleka moyo ku cifanizilo ca cilombo coyamba cija (re 194 ¶26; 195 ¶30-31)
Chiv. 13:16, 17—Musalole kuikidwa cizindikilo ca cilombo (w09 2/15 4 ¶2)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Chiv. 16:13, 14—Kodi mitundu ya anthu idzasonkhanitsidwa bwanji pamodzi “kunkhondo ya tsiku lalikulu la Mulungu Wamphamvuyonse”? (w09 2/15 4 ¶5)
Chiv. 16:21—Ni uthenga wotani umene mosakayikila tidzalengeza, dziko la Satanali likadzangotsala pang’ono kuwonongedwa? (w15 7/15 16 ¶9)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Chiv. 16:1-16 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Woyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi..
Ulendo Wobwelelako Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 2)
Ulendo Wobwelelako Woyamba: (5 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno kambilanani vidiyo yakuti Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji? (koma musaitambitse) (th phunzilo 11)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
• Pitilizani Kusakhala Mbali ya Dziko: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Kusatengako Mbali m’Zandale m’Zocita na m’Zoganiza Zathu. Ndiyeno funsani kuti, kodi mungapewe bwanji kukhala mbali ya dziko pankhani zokhudza cikhalidwe ca anthu kapena ndale za boma? Kenako tambitsani vidiyo yakuti Kusatengako Mbali M’zandale pa Miyambo na Zikondwelelo za Dziko. Ndiyeno funsani kuti, kodi mungakonzekele bwanji mayeselo amene mungakumane nawo okhudza kusalowelela mu zandale?
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 95
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 131 na Pemphelo