CHIVUMBULUTSO 17-19
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU |Nkhondo ya Mulungu Idzathetsa Nkhondo Zonse
19:11, 14-16, 19-21
N’cifukwa ciani Yehova, “Mulungu wacikondi ndi wamtendele” anapatsa Mwana wake amene ni “Kalonga Wamtendele” nchito yomenya nkhondo?—2 Akor. 13:11; Yes. 9:6.
-
Yehova na Yesu amakonda cilungamo ndipo amadana na zoipa
-
Mtendele weni-weni na cilungamo zidzakhalapo kokha ngati anthu oipa acotsedwapo
-
Gulu lankhondo lakumwamba la Mulungu limene ‘likumenya nkhondo mwacilungamo,’ laimilidwa na mahosi oyela, litavala zovala zapamwamba, zoyela bwino, za mbee!
Tingacite ciani kuti tikapulumuke pa nkhondo yapadela imeneyi?—Zef. 2:3