December 30, 2019–January 5, 2020
CHIVUMBULUTSO 20-22
Nyimbo 146 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Taonani! Zinthu Zonse Zimene Ndikupanga N’zatsopano”: (10 min.)
Chiv. 21:1—“Kumwamba kwakale ndi dziko lapansi lakale zinali zitacoka” (re 301 ¶2)
Chiv. 21:3, 4—“Zakalezo zapita” (w13 12/1 11 ¶2-4)
Chiv. 21:5—Lonjezo la Yehova ni lodalilika (w03 8/1 12 ¶14)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Chiv. 20:5—Kodi “akufa enawo” anakhalanso na moyo ku mapeto kwa zaka 1,000 m’lingalilo lotani? (it-2 249 ¶2)
Chiv. 20:14, 15—Kodi “nyanja yamoto” n’ciani? (it-2 189-190)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Chiv. 20:1-15 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Wobwelelako Wacitatu: (3 min. olo kucepelapo) Sankhani mwekha lemba, ndipo gaŵilani mwininyumba kapepa koitanila anthu ku misonkhano. (th phunzilo 3)
Ulendo wobwelelako wacitatu: (4 min. olo kucepelapo) Sankhani mwekha lemba, kenako gaŵilani cofalitsa cophunzitsila Baibo. (th phunzilo 9)
Phunzilo la Baibo: (5 min. olo kucepelapo) jl phunzilo 12 (th phunzilo 6)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Khalani Okonzeka Kusintha Ulaliki”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 97
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 80 na Pemphelo