December 9-15
CHIVUMBULUTSO 10-12
Nyimbo 26 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“‘Mboni Ziŵili’ Zinaphedwa, Kenako Zinakhalanso na Moyo”: (10 min.)
Chiv. 11:3—‘Mboni ziŵili’ zinalosela kwa masiku 1,260 (w14 11/15 30)
Chiv. 11:7—Mbonizo zinaphedwa na “cilombo”
Chiv. 11:11—‘Mboni ziŵili’ zimenezi zinakhalanso na moyo pambuyo pa masiku atatu na hafu
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Chiv. 10:9, 10—Kodi uthenga umene Yohane analandila unali woŵaŵa komanso ‘wonzuna’ motani? (it-2 880-881)
Chiv. 12:1-5—Kodi mawu a pa mavesiwa anakwanilitsidwa bwanji? (it-2 187 ¶7-9)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Chiv. 10:1-11 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 6)
Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo pocita ulaliki wa mwayi wogwilizana na gawo lanu. (th phunzilo 3)
Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani cofalitsa ca mu Thuboksi yathu. (th phunzilo 9)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Dzikolo ‘Linameza Mtsinje’”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Abale ku Korea Atulutsidwa M’ndende.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 94
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 47 na Pemphelo