Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

December 21-27

LEVITIKO 14-15

December 21-27

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Kulambila Koona Kumafuna Kukhala Oyela”: (10 min.)

    • Lev. 15:13-15—Amuna anali kufunika kudziyeletsa ngati adetsedwa (it-1 263)

    • Lev. 15:28-30—Akazi anali kufunika kudziyeletsa ngati adetsedwa (it-2 372 ¶2)

    • Lev. 15:31—Yehova amafuna kuti kulambila kwa anthu ake kuzikhala koyela (it-1 1133)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)

    • Lev. 14:14, 17, 25, 28—Tiphunzilapo ciani tikaganizila zimene zinali kucitika poyeletsa munthu amene anali wakhate? (it-1 665 ¶5)

    • Lev. 14:43-45—Kodi Aisiraeli anaphunzila ciani za Yehova pa lamulo lokhudza khate loopsa la m’nyumba? (g 1/06 14, bokosi)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Lev. 14:1-18 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU