NEHEMIYA 9–11
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU |Olambila Okhulupilika Amacilikiza Dongosolo la Gulu la Mulungu
Anthu a Mulungu anacilikiza kulambila koona ndi mtima wonse m’njila zambili
10:28-30, 32-39; 11:1, 2
-
Aisiraeli anakonzekela ndi kucita Cikondwelelo ca Misasa m’njila yoyenelela.
-
Anthu anali kusonkhana tsiku lililonse kuti amvetsele Cilamulo ca Mulungu cikamaŵelengedwa, ndipo anali kusangalala kwambili.
-
Anthu anali kulapa macimo ao ndi kupemphela kuti Yehova awadalitse.
-
Anthu anavomeleza kucilikiza dongosolo la gulu la Mulungu.
Kucilikiza dongosolo la gulu la Mulungu kunali kuphatikizapo:
-
Kumanga banja ndi anthu okhawo amene anali kulambila Yehova
-
Kupeleka ndalama
-
Kusunga Sabata
-
Kupeleka nkhuni ku guwa lansembe
-
Kupeleka zipatso zoyambilila kuca, ndi mwana woyamba kubadwa wa nyama iliyonse kwa Yehova