Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

February 22-28

NEHEMIYA 12–13

February 22-28
  • Nyimbo 106 ndi Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Zimene Tikuphunzila m’Buku la Nehemiya”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cakuuzimu: (Mph. 8)

    • Neh. 12:31—Kodi kukhala ndi magulu aŵili a oimba nyimbo kunali ndi ubwino wanji? (it-2 454 ndime 1)

    • Neh. 12:31b—Kodi Nehemiya anali kupempha Yehova kuti acite ciani? (w11 2/1 tsa. 14 ndime 3-5)

    • Kodi kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kundiphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ndi mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingagwilitsile nchito mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibulo: Neh. 12:1-26 (Mph. 4 kapena zocepelapo)

KUONJEZELA LUSO LANU MU ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) Gaŵilani kapepala ka ciitano ca ku Cikumbutso kwa munthu amene waonetsa cidwi cocepa.

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 4 kapena zocepelepo) Gaŵilani kapepala ka ciitano ca ku Cikumbutso ndi Nsanja ya Mlonda kwa munthu amene waonetsa cidwi kwambili. Ndiyeno yalani maziko a ulendo wotsatila.

  • Phunzilo la Baibulo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) Fotokozelani amene muphunzila naye Baibulo za Cikumbutso mwa kugwilitsila nchito buku la Zimene Baibo Imaphunzitsa, masamba 206-208. Mungapatse wophunzila wanu thandizo loyenelela kuti adzakwanitse kupezeka pa Cikumbutso.

UMOYO WATHU WACIKRISTU

  • Nyimbo 5

  • Itanilani Aliyense m’Gawo Lanu ku Cikumbutso!”: (Mph. 15) Nkhani yokambilana. Fotokozani mmene mpingo wanu udzafolela gawo lonse. Pokambilana kamutu kakuti “Zimene Muyenela Kucita,” onetsani vidiyo ya Cikumbutso. Limbikitsani onse kuti adzagwile nao nchito yapadela imeneyi ndi kuti adzathandize anthuwo kukulitsa cidwi cao. Citani citsanzo ca mmene tingacitile zimenezi.

  • Phunzilo la Baibulo la Mpingo: ia Mutu 9 ndime 14-24 ndi kubwelelamo pa tsa. 82 (Mph. 30)

  • Bwelezani Mfundo Zimene Taphunzila Komanso Fotokozani Zomwe Tidzaphunzila Mlungu Wotsatila (Mph. 3)

  • Nyimbo 39 ndi Pemphelo