Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

February 20-26

YESAYA 58-62

February 20-26
  • Nyimbo 142 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Ndikalengeze za Caka ca Yehova Cokomela Anthu Mtima”: (10 min.)

    • Yes. 61:1, 2—Yesu anadzozedwa kuti ‘akalengeze za caka ca Yehova cokomela anthu mtima’ (ip-2 peji 322 pala. 4)

    • Yes. 61:3, 4—Yehova wapeleka “mitengo ikulu-ikulu ya cilungamo” kuti icilikize nchito yake (ip-2 peji 326-327 pala. 13-15)

    • Yes. 61:5, 6—“Anthu ocokela kwina” amagwilizana ndi “ansembe a Yehova” pa nchito yaikulu yolalikila nthawi zonse (w12 12/15 peji 25 pala. 5-6)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Yes. 60:17—Ni njila ziti zimene Yehova wakwanilitsila ulosiwu m’masiku otsiliza ano? (w15 7/15 mape. 9-10 mapa. 14-17)

    • Yes. 61:8, 9—Kodi “pangano lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale” n’ciani? Nanga “ana” n’ndani? (w07 1/15 peji 11 pala. 5)

    • Kodi ine pacanga, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwaniphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino zimene ine pacanga ningaseŵenzetse mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Yes. 62:1-12

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 mineti kapena kucepelapo) g17.1 nkhani ya pacikuto

  • Ulendo Wobwelelako: (4 mineti kapena kucepelapo) g17.1 nkhani ya pacikuto

  • Phunzilo la Baibo: (6 mineti kapena kucepelapo)bh peji 16 pala. 19—Ngati n’zotheka, mayi acititse phunzilo kwa mwana wake wamng’ono wamkazi.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 47

  • Seŵenzetsani Mavidiyo mu Ulaliki: (6 min.) Nkhani. Tambitsani vidiyo yakuti Kodi Ufumu wa Mulungu N’ciani? (yendani ku mavidiyo pa MISONKHANO NA UTUMIKI WATHU) Limbikitsani onse kuseŵenzetsa mavidiyo paulendo wawo woyamba kapena wobwelelako pogaŵila zofalitsa za mu March na April.

  • Muziseŵenzetsa Zofalitsa Zanu Mwanzelu(9 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Mmene Zofalitsa Zathu Zimawafikila Anthu mu Congo (yendani ku mavidiyo pa ZIMENE TIMACITA).

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 8 mapa. 14-18, bokosi papeji 85, na bokosi lobwelelamo papeji 86

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 114 na Pemphelo