February 27– March 5
YESAYA 63-66
Nyimbo 19 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Kumwamba Kwatsopano ndi Dziko Lapansi Latsopano Zidzabweletsa Cisangalalo Cacikulu”: (10 min.)
Yes. 65:17—“Zinthu zakale sizidzakumbukilidwanso” (ip-2 peji. 383 pala. 23)
Yes. 65:18, 19—Padzakhala cisangalalo cacikulu (ip-2 peji 384 pala. 25)
Yes. 65:21-23—Umoyo udzakhala wokhutilitsa, ndipo anthu adzakhala otetezeka (w12 9/15 peji 9 mapala. 4-5)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Yes. 63:5—Kodi mkwiyo wa Mulungu umam’cilikiza bwanji? (w07 1/15 peji 11 pala. 6)
Yes. 64:8—Kodi Yehova amaseŵenzetsa bwanji mphamvu zake monga Wotiumba? (w13 6/15 25 mapala. 3-5)
Kodi ine pacanga, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwaniphunzitsa ciani za Yehova?
Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino zimene ine pacanga ningaseŵenzetse mu ulaliki?
Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Yes. 63:1-10
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (2 mineti kapena kucepelapo) Aef. 5:33—Phunzitsani Coonadi.
Ulendo Wobwelelako: (4 mineti kapena kucepelapo) 1 Tim. 5:8; Tito 2:4, 5—Phunzitsani Coonadi.
Nkhani: (6 mineti kapena kucepelapo) Yes. 66:23; w06 11/1 peji 30-31 pala. 14-17—Mutu: Kusonkhana—Mbali Yosatha ya Kulambila Kwathu
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
‘Kondwelani mu Ciyembekezo Canu’ (Yes. 65:17, 18; Aroma 12:12) (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Kondwelani ndi Ciyembekezo (yendani ku mavidiyo pa BAIBULO)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 9 pala. 1-9, ndi chati papeji 89”
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 95 na Pemphelo