Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

February 12-18

MATEYU 14-15

February 12-18
  • Nyimbo 93 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Kudyetsa Anthu Ambili Mwa Kugwilitsila Nchito Anthu Ocepa”: (10 min)

    • Mat. 14:16, 17—Ophunzila anali cabe na mitanda isanu ya mkate na nsomba ziŵili (w13 7/1 peji 21 pala. 2)

    • Mat. 14:18, 19—Yesu anadyetsa khamu la anthu mwa kuseŵenzetsa ophunzila ake (w13 7/1 peji 21 pala. 3)

    • Mat. 14:20, 21—Anthu masauzande anapindula na cozizwitsa ca Yesu (nwtsty mfundo younikila pa Mat. 14:21; w13 7/1 peji 21 pala. 1)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Mat. 15:7-9—N’cifukwa ciani tifunika kupewa kucita zacinyengo? (nwtsty mfundo younikila)

    • Mat. 15:26—Kodi Yesu ayenela kuti anatanthauza ciani pamene anaseŵenzetsa mau akuti “tiagalu”? (nwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mat. 15:1-20

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano a citsanzo.

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Woyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Nkhani: (6 min. olo kucepelapo) w15 9/15 mape. 19-20 mapa. 14-17—Mutu: Kuyang’anitsitsa Yesu Kudzalimbitsa Cikhulupililo Canu.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 135

  • Khala Bwenzi la YehovaKupanga Mabwenzi: (7 min.) Tambitsani vidiyo imeneyi. Pambuyo pake, itanani ana amene munasankha kuti abwele ku pulatifomu, na kuwafunsa mafunso aya: N’cifukwa ciani mufunika kupanga ubwenzi na anthu okonda Yehova? Nanga mungaphunzile ciani kwa iwo?

  • Uzilemekeza Atate Ako ndi Amayi Ako”: (8 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo ya tukadoli yakuti Ningakambe Nawo Bwanji Makolo Anga?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 8

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 148 na Pemphelo