Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

February 19-25

MATEYU 16-17

February 19-25
  • Nyimbo 45 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Kodi Muli na Maganizo a Ndani?”: (10 min.)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Mat. 16:18—N’ndani anali thanthwe limene Yesu anamangapo mpingo wacikhristu? (nwtsty mfundo younikila)

    • Mat. 16:19—Kodi “makiyi a Ufumu wakumwamba” amene Yesu anapatsa Petulo n’ciani? (nwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mat. 16:1-20

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano a citsanzo. Ndiyeno, yankhani pa zimene anthu a m’gawo lanu amakamba posafuna kulalikidwa.

  • Ulendo Wobwelelako Woyamba: (3 min. olo kucepelelapo) Seŵenzetsani makambilano a citsanzo.

    Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyo.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU