Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MATEYU 16-17

Kodi Muli na Maganizo a Ndani?

Kodi Muli na Maganizo a Ndani?

16:21-23

  • Ngakhale kuti mwina Petulo anali kukamba ali na zolinga zabwino, Yesu sanazengeleze kumuwongolela pa kaganizidwe kake kolakwika.

  • Yesu anadziŵa kuti imeneyo siinali nthawi yakuti ‘adzikomele mtima.’ Mosakayikila, Satana ndiye anali kufuna kuti Yesu adzikomele mtima panthawi yovuta ngati imeneyo.

16:24

Yesu anachula zinthu zitatu zotithandiza kukwanilitsa cifunilo ca Mulungu. Kodi ciliconse ca zinthuzi citanthauza ciani?

  • Kudzikana wekha:

  • Kunyamula mtengo wako wozunzikilapo:

  • Kutsatila Yesu mosalekeza: