Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

February 26–March 4

MATEYU 18-19

February 26–March 4
  • Nyimbo 121 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Muzisamala Kuti Musadzipunthwitse Kapena Kupunthwitsa Ena”: (10 min.)

    • Mat. 18:6, 7—Sitiyenela kupunthwitsa ena (nwtsty mfundo zounikila na zithunzi)

    • Mat. 18:8, 9—Tiyenela kupewa ciliconse cimene cingatipangitse kupunthwa (nwtsty mfundo younikila, “Gehena”)

    • Mat. 18:10—Yehova amadziŵa tikapunthwitsa ena (nwtsty mfundo younikila; w10 11/1 peji 16)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Mat. 18:21, 22—Kodi tiyenela kukhululukila m’bale wathu nthawi zingati? (nwtsty mfundo younikila)

    • Mat. 19:7—Kodi colinga ca ‘kalata yothetsa cikwati’ cinali ciani? (nwtsty mfundo younikila na zithunzi)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mat. 18:18-35

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano a citsanzo.

  • Ulendo Wobwelelako Wacitatu: (3 min. olo kucepelapo) Sankhani mwekha lemba na kugaŵila cofalitsa cophunzitsila Baibo.

  • Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) bhs peji 26 mapa. 18-20—Onetsani mmene mungamufikile pamtima.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 90

  • Musakhale Cokhumudwitsa (2 Akor. 6:3): (9 min.) Tambitsani vidiyo.

  • Kampeni Yoitanila Anthu Ku Cikumbutso Idzayamba pa March 3: (6 min.) Nkhani yozikidwa pa Kabuku ka Umoyo na Utumiki ka February 2016 peji 8. Gaŵilani kapepa koitanila anthu ku cikumbutso kwa aliyense m’gulu, na kukambilana zimene zilimo. Gogomezani kuti nkhani yapadela ya mutu wakuti, “Kodi Yesu Khristu Ndani Maka-maka?” idzakambiwa wiki ya March 19, 2018. Nkhaniyi idzatithandiza kuyembekezela mwacidwi tsiku la Cikumbutso. Fotokozani zimene mpingo wakonza kuti ukathe kufola gawo lonse.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 10, na bokosi pa peji 28

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 133 na Pemphelo