Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Mafanizo a Ufumu na Tanthauzo Lake Kwa Ise

Mafanizo a Ufumu na Tanthauzo Lake Kwa Ise

Yesu anaseŵenzetsa mafanizo osavuta kumva pophunzitsa mfundo zozama za coonadi. Komabe, ni anthu odzicepetsa okha amene amamvetsetsa na kuseŵenzetsa zimene iye anaphunzitsa. (Mat. 13:10-15) Pa fanizo lililonse la Ufumu, yankhani mafunso otsatilawa: Kodi ningapindule bwanji na fanizoli? Nanga linganithandize bwanji mu umoyo wanga?

UFUMU WAKUMWAMBA ULI NGATI . . .