Aona cilengedwe ca Yehova ku Switzerland

UMOYO NA UTUMIKI WATHU–KABUKU KA MISONKHANO February 2019

Makambilano Acitsanzo

Makambilano otsatizana-tsatizana ofotokoza za kukhala mabwenzi.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Pitilizani Kuphunzitsa Cikumbumtima Canu

Cikumbumtima cathu cingatithandize ngati ticiphunzitsa mfundo za m’Baibo.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Kodi Mumawaona Makhalidwe Osaoneka a Mulungu?

Cilengedwe cotizungulila cimaonetsa mphamvu za Yehova, cikondi, nzelu, cilungamo, na kuwolowa manja kwake.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Mulungu Akuonetsa Cikondi Cake Kwa Ife”

Kodi tingaonetse bwanji kuti timayamikila mphatso ya dipo?

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Mukuyembekezela Mwacidwi?

Mungaonetse bwanji kuti ndimwe okonzeka pamene mukuyembekezela ‘kuonekela kwa ana a Mulungu’?

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Pitilizani Kuyembekezela Mopilila

N’ciani cingatithandize kuyembekezela mwacidwi olo tikumane na mavuto?

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Fanizo la Mtengo wa Maolivi

Kodi mbali zosiyana-siyana za mtengo wophiphilitsa wa maolivi ziimila ciani?

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Kunola luso lathu mu ulaliki—Kuleka kutsogoza maphunzilo a baibo osapita patsogolo

Tingacite ciani ngati wophunzila Baibo sapita patsogolo pambuyo pakuti taphunzila naye kwa nthawi yaitali?