Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

February 11-17

AROMA 4-6

February 11-17
  • Nyimbo 20 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Mulungu Akuonetsa Cikondi Cake Kwa Ife”: (10 min.)

    • Aroma 5:8, 12—Yehova anationetsa cikondi “pamene tinali ocimwa” (w11 6/15 peji 12 pala. 5)

    • Aroma 5:13, 14—Ucimo na imfa zinalamulila monga mfumu (w11 6/15 peji 12 pala. 6)

    • Aroma 5:18, 21—Yehova anatumiza mwana wake kuti tilandile moyo (w11 6/15 mape. 12-13 mapa. 9-10)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Aroma 6:3-5—Kodi kubatizidwa “mu mgwilizano ndi Khristu Yesu” komanso kubatizidwa “mu imfa yake,” kukutanthauza ciani? (w08 6/15 peji 29 pala. 7)

    • Aroma 6:7—N’cifukwa ciani oukitsidwa sadzaweluzidwa mogwilizana na macimo amene anacita akalibe kufa? (w14 6/1 peji 11 pala. 1)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Aroma 4:1-15 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI]

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 107

  • Zofunikila za Mpingo: (15 min.)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 54

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 97 na Pemphelo