February 18-24
AROMA 7-8
Nyimbo 27 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Mukuyembekezela Mwacidwi?”: (10 min.)
Aroma 8:19—Posacedwa “ana a Mulungu” adzaonekela (w12 7/15 peji 11 pala. 17)
Aroma 8:20—“Cilengedwe cinapelekedwa ku mkhalidwe wopanda pake . . . pa maziko a ciyembekezo” (w12 3/15 peji 23 pala. 11)
Aroma 8:21—Cilengedwe “cidzamasulidwa ku ukapolo wa kuvunda” (w12 3/15 peji 23 pala. 12)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Aroma 8:6—Kodi pali kusiyana kotani pakati pa “kuika maganizo pa zinthu za thupi” na “kuika maganizo pa zinthu za mzimu”? (w17.06 peji 3))
Aroma 8:26, 27—Kodi Yehova amayankha bwanji ‘madandaulo amene sitingathe kuwafotokoza’? (w09 11/15 peji 7 pala. 20)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Aroma 7:13-25 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Kubwelelako Koyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Kubwelelako Koyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 6)
Kubwelelako Koyamba: (5 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Kenako chulani na kukambilana vidiyo yakuti Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji? (Koma musaitambitse vidiyoyi) (th phunzilo 9)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Pitilizani Kuyembekezela Mopilila”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Tifunika “Kuthamanga Mopilila”—Khalani na Cidalilo Cakuti Mudzalandila Mphoto.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 55
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 124 na Pemphelo