AROMA 7-8
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU |Kodi Mukuyembekezela Mwacidwi?
8:19-21
-
“Cilengedwe”: anthu amene ali na ciyembekezo cokakhala padziko lapansi
-
‘Kuonekela kwa ana a Mulungu’: nthawi pamene odzozedwa adzathandiza Khristu kuwononga dongosolo loipa la Satana
-
“Maziko a ciyembekezo”: lonjezo la Yehova lotipulumutsa kupitila mu imfa ya Yesu na kuukitsidwa kwake
-
‘Kumasulidwa ku ukapolo wa kuvunda’: kumasulidwa pang’ono-pang’ono kucoka ku ucimo na imfa