Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

February 4-10

AROMA 1-3

February 4-10
  • Nyimbo 88 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Pitilizani Kuphunzitsa Cikumbumtima Canu”: (10 min.)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Aroma 3:4—Kodi timalola bwanji ‘Mulungu kukhala wonena zoona’? (w08 6/15 peji 30 pala. 5)

    • Aroma 3:24, 25—Kodi “dipo lolipilidwa ndi Khristu Yesu” linaphimba bwanji “macimo amene anacitika kale”? (w08 6/15 peji 29 pala. 6)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Aroma 1:1-17 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa: (10 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Kukambilana Mwacibadwa, ndiyeno kambilanani phunzilo 2 m’kabulosha kakuti Kuphunzitsa.

  • Nkhani: (5 min. olo kucepelapo) w06 6/1 mape. 12-13—Mutu: Muziona Moyenela Zimene Simungakwanitse Kucita na Zimene Ena Sangakwanitse Kucita. (th phunzilo 7)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU