Alalikila uthenga wabwino ku Ghana

UMOYO NA UTUMIKI WATHU–KABUKU KA MISONKHANO January 2017

Maulaliki a citsanzo

Maulaliki ogaŵila Nsanja ya Mlonda, ndi ophunzitsila coonadi cokhudza masiku otsiliza. Seŵenzetsani mfundozi kukonza maulaliki anu.

CUMA COCOKELA M’MAU A MULUNGU

Yehova Amasamalila Anthu Ake

Mofanana ndi munthu wolandila alendo mooloŵa manja, Yehova amatigaŵila cakudya cauzimu ca mwana alilenji.

CUMA COCOKELA M’MAU A MULUNGU

“Mfumu Idzalamulila Mwacilungamo”

Yesu, Mfumuyo, imapeleka akulu kuti asamalile nkhosa. Iwo amabweletsa mpumulo pozitsogolela na kuzitsitsimula mwauzimu.

CUMA COCOKELA M’MAU A MULUNGU

Hezekiya anafupidwa cifukwa ca cikhulupililo cake

Asuri anayesa kuyofya Ayuda kuti angodzipeleka osamenyana nawo, koma Yehova anatumiza mngelo kuti akateteze Yerusalemu.

UMOYO WACIKHIRISTU

“Inu Mulungu Wanga, Cikhulupililo Canga Cili mwa Inu”

Tifunika kudalila Yehova Mulungu pamene zinthu zili bwino komanso panthawi yovuta. Kodi Hezekiya anaonetsa bwanji kuti anadalila Mulungu?

CUMA COCOKELA M’MAU A MULUNGU

Yehova Amapatsa Mphamvu Munthu Wotopa

Kuuluka kwa nkhwazi kumaonetsa bwino mmene mphamvu za Mulungu zimatithandizila kusaleka kum’lambila.

UMOYO WACIKHIRISTU

Kumbukilani Kupemphelela Akhiristu Amene Akuzunzidwa

Kodi tingawapemphelele ciani Akhiristu amene akuzunzidwa?

CUMA COCOKELA M’MAU A MULUNGU

Maulosi Onse a Yehova Amakwanilitsika

Pafupi-fupi zaka 200 Babulo akalibe kugonjetsewa, Yehova anakambilatu, kupitila mwa mneneli Yesaya, zimene zidzacitika.